Praise Umali - Ameni (Official Music Video)
Leírás
My new album “Dreams For Sale" is Out Now! You can listen here https://onerpm.link/DreamsForSale
Lyrics
Ngati mwalemba ameni
Zikhale choncho ameni
Tivomeleza ameni
Mitima ikuwawa ameni
Inu Ngati mwalola ameni
Zikhale choncho ameni
Ife tivomeleza ameni
Olo mitima ikuwawa ameni
Kodi simmationa?
Mbuye simmatikonda?
Timadabwa
Timakhala ndi mafunso
Onani tikulira pano
Makolo akulira pano
Poti ayamba kupita ndi ana awo
Makolo akwilira bwanji Ana awo?
Ambuye kodi simmationa?
Kapena simmatikonda?
Ife timadabwa
Timakhala ndi mafunso
Koma ngati mwalemba ameni
Zikhale choncho ameni
Tivomeleza ameni
Mitima ikuwawa ameni
Inu Ngati mwalola ameni
Zikhale choncho ameni
Ife tivomeleza ameni
Olo mitima ikuwawa ameni
Ngati mwalemba ameni
(Poti mwalora Jah Jah)
Zikhale choncho ameni
(Umo mmene mufunilamotu baba)
Tivomeleza ameni
(Mwina tizazindikila patsogolo)
Mitima ikuwawa ameni
(Mwina tizazindikila patsogolo)
Inu Ngati mwalola ameni
Zikhale choncho ameni
Ife tivomeleza ameni
(Mwina tizazindikila patsogolo)
Olo Mitima ikuwawa ameni
(Mwina tizazindikila patsogolo)
Poti mwalora ameni
Ameni ameni ameni
Ameni ameni
Ameni ameni ameni
Zimavuta kunena ameni
Zutivuta kunena ameni
Mbuye tikondeni
Ameni
Ngati mwalemba ameni
Zikhale choncho ameni
Tivomeleza ameni
Mitima ikuwawa ameni
Inu Ngati mwalola ameni
Zikhale choncho ameni
Ife tivomeleza ameni
Olo mitima ikuwawa ameni
Praise Umali - Ameni (Official Music Video) – Online videóklip leírása
Nézd meg a(z) Praise Umali - Ameni (Official Music Video) című zenei videót kiváló minőségben online a videok.top-on! Hallgasd meg a legújabb slágereket és kövesd kedvenc előadóid hivatalos videóklipjeit regisztráció nélkül. Böngéssz a zenei kategóriák között, és fedezd fel a legfrissebb hazai és nemzetközi újdonságokat, koncerteket és dalokat nálunk.
Zenei poén betöltése...






![MeerFly - "HAA TEPOK" (Ft. Kidd Santhe & MK) [OFFICIAL MUSIC VIDEO] // MALAYSIAN MUSIC REACTION](https://i.ytimg.com/vi/nDgNUsxxCYo/hqdefault.jpg)



























![คุยไปก่อน - CAPTAIN [Official Music Video] | Nadao Music](https://i.ytimg.com/vi/xwnl3E6T3Vg/hqdefault.jpg)


![ดี๊ดี (UNEXPECTED) - JAYLERR x PARIS [Official Music Video] | Nadao Music](https://i.ytimg.com/vi/-SEmqYTbm4Q/hqdefault.jpg)







































![Audiosoulz feat. KAZADI – Let The Music Play [Official Music Video]](https://i.ytimg.com/vi/Ihdj1GqtSK0/hqdefault.jpg)

![ela tv - Nahom Yohannes ( Meste ) - Freweini - New Eritrean Music 2019 - [ Official Music Video ]](https://i.ytimg.com/vi/v6Zq9BWOXuY/hqdefault.jpg)































































![veszélyes coronita mix 2020 [DJ Renáto]](https://i.ytimg.com/vi/3iCRPFs95mw/hqdefault.jpg)



















































